Show notes
Monga ana womvera wosadzifanizitsanso ndi zilakolako zakale, pokhala wosadziwa inu: Komatu monga Iye wakuyitana inu ali woyera mtima, khalani inunso woyera mtima m’makhalidwe anu onse: Popeza kwalembedwa, mudzikhala woyera mtima, pakuti Ine ndine woyera mtima: (1Pe

